Get Clarity, Not Just Headlines.
Published loading...Updated

Nthambi ya za Nyengo alosera mvula yochuluka mnyengo ya mchaka chino ndi cha mawa

Summary by Nyasa Times
Nthambi yowona za Nyengo ndi kusintha kwa Nyengo mdziko muno yalosera nyengo la dzinja mchaka chino ndi cha mawa (2024/2025) kuti kukhala mvula yochuluka poyelekeza ndi dzinja lapitali. Mkulu woyang’anira nthambiyi, a Lucy Mtilatila awuza atolankhani mu mzinda wa Lilongwe la chisanu kuti ngakhale zili chomwechi, Pali chiyembekezo chakuti mwezi wa November utha kukhala ndi […] The post Nthambi ya za Nyengo alosera mvula yochuluka mnyengo ya mchak…
DisclaimerThis story is only covered by news sources that have yet to be evaluated by the independent media monitoring agencies we use to assess the quality and reliability of news outlets on our platform. Learn more here.

Bias Distribution

  • There is no tracked Bias information for the sources covering this story.
Factuality

To view factuality data please Upgrade to Premium

Ownership

To view ownership data please Upgrade to Vantage

Nyasa Times broke the news in Malawi on Monday, September 16, 2024.
Sources are mostly out of (0)