Boma lachotsa mlandu wa anthu osokoneza m'dipiti wamtsogoleri Malawi 24 | Latest News from Malawi
Summary by Malawi 24
1 Articles
1 Articles
All
Left
Center
Right
Boma lachotsa mlandu wa anthu osokoneza m'dipiti wamtsogoleri Malawi 24 | Latest News from Malawi
Boma lalengeza kuti lathetsa mlandu wa anthu atatu omwe anawanjata kamba kosokoneza galimoto zapa m’dipiti wa mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera pomwe ankakakwera ndege ku Chileka mu mzinda wa Blantyre. Omwe amazengedwa mulanduwu ndi a Pearson Chimimba azaka 48, a Lucy Namba azaka 48 komanso a Hector Ndawala azaka 38 zakubadwa. Anthu atatuwa […] The post Boma lachotsa mlandu wa anthu osokoneza m’dipiti wamtsogoleri appeared first on Mal…
·Malawi
Read Full ArticleCoverage Details
Total News Sources1
Leaning Left0Leaning Right0Center0Last UpdatedBias DistributionNo sources with tracked biases.
Bias Distribution
- There is no tracked Bias information for the sources covering this story.
Factuality
To view factuality data please Upgrade to Premium
Ownership
To view ownership data please Upgrade to Vantage