Kampani ya Nation Publications Limited (NPL) ndi abwenzi ake anapeza K672 miliyoni pa liwiro la msangulutso (Mothers Fun Run) lomwe lidachitika memzinda wa Mzuzu Loweruka lapitalo. BRIGHT KUMWENDA adacheza ndi mkulu wa NPL komanso wa MFR a Mbumba Banda kati amve zambiri. Banda: Tiyeni tigwirane manja Mothers Fun Run (MFR) ya chaka chino yapeza K672 ...
This story is only covered by news sources that have yet to be evaluated by the independent media monitoring agencies we use to assess the quality and reliability of news outlets on our platform. Learn more here.