Skip to main content
See every side of every news story
Published • loading... • Updated

Apolisi Agwira Anthu Awiri Pa Nkhani Ya Kupha Mtsikana Wa Zaka 19 Ku Mzuzu

Summary by 247malawi.com
Wolemba: Chisomo Phiri Apolisi mumzinda wa Mzuzu agwira anthu awiri omwe akuwaganizira kuti akukhudzidwa ndi kuphedwa kwa mtsikana wa zaka 19, yemwe thupi lake linapezeka m'mbali mwa msewu wa Zolozolo-Recreation, pafupi ndi bwalo la Mzuzu Upper Stadium pa 24 October 2026. M’mawu ake,wachiwiri kwa wolankhulira apolisi pa siteshoni ya Mzuzu, Edson Chipeni, watchula anthu […]
DisclaimerThis story is only covered by news sources that have yet to be evaluated by the independent media monitoring agencies we use to assess the quality and reliability of news outlets on our platform. Learn more here.

1 Articles

Wolemba: Chisomo Phiri Apolisi mumzinda wa Mzuzu agwira anthu awiri omwe akuwaganizira kuti akukhudzidwa ndi kuphedwa kwa mtsikana wa zaka 19, yemwe thupi lake linapezeka m'mbali mwa msewu wa Zolozolo-Recreation, pafupi ndi bwalo la Mzuzu Upper Stadium pa 24 October 2026. M’mawu ake,wachiwiri kwa wolankhulira apolisi pa siteshoni ya Mzuzu, Edson Chipeni, watchula anthu […]

Think freely.Subscribe and get full access to Ground NewsSubscriptions start at $9.99/yearSubscribe

Bias Distribution

  • There is no tracked Bias information for the sources covering this story.

Factuality Info Icon

To view factuality data please Upgrade to Premium

Ownership

Info Icon

To view ownership data please Upgrade to Vantage

247malawi.com broke the news on Thursday, November 12, 2026.
Too Big Arrow Icon
Sources are mostly out of (0)
News
Feed Dots Icon
For You
Search Icon
Search
Blindspot LogoBlindspotLocal