This article was originally published on Malawi24">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform.
Kuli chimwemwe kwa alimi pafupifupi 50,000 m’boma la Kasungu pomwe makoponi pansi pa ndondomeko ya zipangizo za ulimi zotsika mtengo ya Farm Inputs Subsidy Program (FISP), afika tsopano. Boma la Kasungu lalandira makoponi omwe alimi okwana 48,596 omwe adalembetsedwa agwiritse ntchito pogulira feteleza mu ndondomeko ya FISP. A Loveness Kapachika om…
This story is only covered by news sources that have yet to be evaluated by the independent media monitoring agencies we use to assess the quality and reliability of news outlets on our platform. Learn more here.