Boma lauza apolisi kuti amange anthu omwe anazula mipando ku Bingu Malawi 24 | Latest News from Malawi
Summary by Malawi 24
1 Articles
1 Articles
All
Left
Center
Right
Boma lauza apolisi kuti amange anthu omwe anazula mipando ku Bingu Malawi 24 | Latest News from Malawi
Nduna ya zamasewero Uchizi Mkandawire yapempha apolisi kuti afufuze anthu omwe awononga mipando yoposa 200 ku bwalo la zamasewero la Bingu ku Lilongwe A Mkandawire ayankhula izi atayendera bwalo la zamasewero la Bingu komwe anthu anazula mipando 239 pomwe anakaonela mpira wa pakati pa Silver Strikers ndi Mighty Wanderers. Iwo anati apolisi agwire ntchito yawo […] The post Boma lauza apolisi kuti amange anthu omwe anazula mipando ku Bingu appeare…
·Malawi
Read Full ArticleCoverage Details
Total News Sources1
Leaning Left0Leaning Right0Center0Last UpdatedBias DistributionNo sources with tracked biases.
Bias Distribution
- There is no tracked Bias information for the sources covering this story.
Factuality
To view factuality data please Upgrade to Premium
Ownership
To view ownership data please Upgrade to Vantage