Yawo ija angoni: fisi wapangidwa ndiwo ku Ntcheu Malawi 24 | Latest News from Malawi
Summary by Malawi 24
1 Articles
1 Articles
All
Left
Center
Right
Yawo ija angoni: fisi wapangidwa ndiwo ku Ntcheu Malawi 24 | Latest News from Malawi
Sadyeka uja lero wadyeka: Angoni a ku Ndagoma m’boma la Ntcheu adodometsa gulu pomwe achita ndiwo fisi yemwe wakhala akuwathera mbuzi m’mudzimo. Izi ndi malingana ndi kanema ina yomwe anthu akugawana m’masamba a mchezo yomwe ikuwonetsa azibambo angapo akuwawura fisi yemwe anamupha m’bandakucha wa lolemba pa 2 October. Izi zachitika m’mudzi wa Ndagoma omwe uli […] The post Yawo ija angoni: fisi wapangidwa ndiwo ku Ntcheu appeared first on Malawi …
·Malawi
Read Full ArticleCoverage Details
Total News Sources1
Leaning Left0Leaning Right0Center0Last UpdatedBias DistributionNo sources with tracked biases.
Bias Distribution
- There is no tracked Bias information for the sources covering this story.
Factuality
To view factuality data please Upgrade to Premium
Ownership
To view ownership data please Upgrade to Vantage