Samalani uko! A ma truck aopseza kuti anyanyalanso ntchito Malawi 24 | Latest News from Malawi
Summary by Malawi 24
1 Articles
1 Articles
All
Left
Center
Right
Samalani uko! A ma truck aopseza kuti anyanyalanso ntchito Malawi 24 | Latest News from Malawi
Palibe kopumira. Ngati a boma akuti mafuta akusowa chifukwa palibe ndalama za kunja, pompano aonjezekera kusowa chifukwa sipakhala owanyamula. Onse oyendetsa galimoto zikuluzikulu ati kuyambira pa 18 apa ayamba kunyanyala ntchito. Malinga ndi Malipoti, madalayivalawa ati ndi osakondwa kuti mavuto amene akhala akukumana nawo sanakonzedwe ndipo ena angoonjezekera. Mtsogoleri wa bungwe loyang’anira madalayivalawa a Mphatso […] The post Samalani uko…
·Malawi
Read Full ArticleCoverage Details
Total News Sources1
Leaning Left0Leaning Right0Center0Last UpdatedBias DistributionNo sources with tracked biases.
Bias Distribution
- There is no tracked Bias information for the sources covering this story.
Factuality
To view factuality data please Upgrade to Premium
Ownership
To view ownership data please Upgrade to Vantage