Published

Phungu wa UTM Susan Dosi akuti: “Kodi nkachoka ku boma kupita ku opposition, zipindulira ndani?”

Summary by Nyasa Times
Phungu wa Chikwawa West a Susan Dossi, yemwe anawina ngati phungu oyima payekha kenako nkulowa UTM, wati chipanichi sichinamufikire ndi uthenga woti achoke ku mbali ya boma kupita yotsutsa boma. A Dossi ati ngakhale chipanichi chitawafikira, sakuona phindu lochoka mbali ya boma chifukwa anthu kudera lawo akufuna chitukuko chomwe chimachokanso kuboma komweko. “Kodi nkachoka ku […] The post Phungu wa UTM Susan Dosi akuti: “Kodi nkachoka ku boma ku…
Think freely.Subscribe and get full access to Ground NewsSubscriptions start at $9.99/yearSubscribe

Bias Distribution

  • There is no tracked Bias information for the sources covering this story.
Factuality

To view factuality data please Upgrade to Premium

Ownership

To view ownership data please Upgrade to Vantage

Sources are mostly out of (0)

You have read out of your 5 free daily articles.

Join us as a member to unlock exclusive access to diverse content.