Published

Matako apatsidwa chilango chogwira ntchito zosalipidwa  Malawi 24 | Latest News from Malawi

Summary by Malawi 24
Bwalo la Senior Resident Magistrate Joshua Nkhono ku Balaka lalamula kuti a Lilian Matako komanso a Ishmael Chitete akagwire ntchito zosalipidwa m’dera lawo atapezeka olakwa pa mlandu ovulaza munthu mwadala. Awiriwa adamangidwa zitadziwika kuti adapeleka chilango chomumangilira mumtengo mwana wa zaka zisanu ndi zinayi, Mercy Magombo, komanso kumuthira madzi a chitedze kaamba komuganizira kuti adaba […] The post Matako apatsidwa chilango chogwira…
Think freely.Subscribe and get full access to Ground NewsSubscriptions start at $9.99/yearSubscribe

Bias Distribution

  • There is no tracked Bias information for the sources covering this story.
Factuality

To view factuality data please Upgrade to Premium

Ownership

To view ownership data please Upgrade to Vantage

Sources are mostly out of (0)

You have read out of your 5 free daily articles.

Join us as a member to unlock exclusive access to diverse content.