Katelele Ching'oma watisiya Malawi 24 | Latest News from Malawi
1 Articles
1 Articles
Katelele Ching'oma watisiya Malawi 24 | Latest News from Malawi
M’modzi mwa oyimba odziwika bwino kuno ku Malawi, Katelele Ching’oma, watisiya. Oyimbayu wamwalira m’bandakucha wa lero ku chipatala cha Kamuzu Central ku Lilongwe komwe anamutengela. Mchimwene wake wa oyimbayu, a Elvis Ching’oma, wati Katelele amadwala nthenda yokhudza chiwindi. Moses Makawa, yemwe anali mnzake wa Katelele wati oyimbayu anagonekedwa ku chipatala masiku atatu apitawa. “Amadwala inde […] The post Katelele Ching’oma watisiya appea…
Coverage Details
Bias Distribution
- There is no tracked Bias information for the sources covering this story.
To view factuality data please Upgrade to Premium
Ownership
To view ownership data please Upgrade to Vantage