This article was originally published on Malawi24">Malawi24, Malawi's #1 independent news platform.
Pomwe kwa ena ndi mwikho, ambiri maka pa masamba amchezo ati sakuwonapo vuto ndi zomwe ikuchita njonda ina ku Dowa yomwe ikukumbiratu dzenje lomwe anthu ambiri safuna ataliwona. Faidoni Benamu Kalitsiro wazaka 78, wadodometsa anthu pomwe wayamba ntchito yokumba manda ake m’mudzi wa Makwani m’dera la mfumu yayikulu Dzoole m’bomali. Benamu Kalitsiro…
This story is only covered by news sources that have yet to be evaluated by the independent media monitoring agencies we use to assess the quality and reliability of news outlets on our platform. Learn more here.