Skip to main content
See every side of every news story
Published • loading... • Updated

Akusaka Wopha Malume Chifukwa Cha Mtengo

Summary by The Nation
Apolisi ku Chiradzulu akufunafuna bambo wa zaka 35 a Michael Mkandawire,  powaganizira kuti adamenya malume ake a zaka 65, a Rodrick Michael, mpaka kufa pa mkangano wokhudza mtengo wa mango. Izi zidachitika pa 24 October 2026 m’mudzi wa Nanyanga, m’dera la T/A Likoswe, malinga ndi wachiwiri kwa mneneri wa polisi ku Chiradzulu a Andrew Kusimbwa. …
DisclaimerThis story is only covered by news sources that have yet to be evaluated by the independent media monitoring agencies we use to assess the quality and reliability of news outlets on our platform. Learn more here.

1 Articles

Apolisi ku Chiradzulu akufunafuna bambo wa zaka 35 a Michael Mkandawire,  powaganizira kuti adamenya malume ake a zaka 65, a Rodrick Michael, mpaka kufa pa mkangano wokhudza mtengo wa mango. Izi zidachitika pa 24 October 2026 m’mudzi wa Nanyanga, m’dera la T/A Likoswe, malinga ndi wachiwiri kwa mneneri wa polisi ku Chiradzulu a Andrew Kusimbwa. …

·Blantyre, Malawi
Read Full Article
Think freely.Subscribe and get full access to Ground NewsSubscriptions start at $9.99/yearSubscribe

Bias Distribution

  • There is no tracked Bias information for the sources covering this story.

Factuality Info Icon

To view factuality data please Upgrade to Premium

Ownership

Info Icon

To view ownership data please Upgrade to Vantage

The Nation broke the news in Blantyre, Malawi on Sunday, November 1, 2026.
Too Big Arrow Icon
Sources are mostly out of (0)
News
Feed Dots Icon
For You
Search Icon
Search
Blindspot LogoBlindspotLocal