A Tembo anali munthu wabwino osati zochotsana muchipani akupanga a Mutharika - Dausi Malawi 24 | Latest News from Malawi
Summary by Malawi 24
1 Articles
1 Articles
All
Left
Center
Right
A Tembo anali munthu wabwino osati zochotsana muchipani akupanga a Mutharika - Dausi Malawi 24 | Latest News from Malawi
Olira samugwira pakamwa ndipo mneneri wakale wa chipani chotsutsa cha DPP, a Nicholas Dausi, walira mokweza pa mwambo wa maliro wa a John Tembo. Poyankhula pa bwalo la za masewero la Dedza pamene amaimilira anzawo a Kondwani Nankhumwa amene ndi mtosgoleri otsutsa mu nyumba ya malamulo, A Dausi anati a Tembo anali katakwe pa ndale. […] The post A Tembo anali munthu wabwino osati zochotsana muchipani akupanga a Mutharika – Dausi appeared first on …
·Malawi
Read Full ArticleCoverage Details
Total News Sources1
Leaning Left0Leaning Right0Center0Last UpdatedBias DistributionNo sources with tracked biases.
Bias Distribution
- There is no tracked Bias information for the sources covering this story.
Factuality
To view factuality data please Upgrade to Premium
Ownership
To view ownership data please Upgrade to Vantage