News from Peter Mutharika
Media Bias Breakdown
How is the media covering Peter Mutharika?Peter Mutharika often is covered by Center Media sources.
Center: 100%
Stay current with all the latest and breaking news about Peter Mutharika, compare headlines and perspectives between news sources on stories happening today. In total, 31 stories have been published about Peter Mutharika which Ground News has aggregated in the past 3 months.
Location of Coverage About Peter MutharikaBased on 31 recent stories
0% Local Coverage96% National Coverage4% International Coverage
Media Bias Breakdown
How is the media covering Peter Mutharika?Peter Mutharika often is covered by Center Media sources.
Center: 100%
Top Peter Mutharika News
Latest News Stories
Peter Mutharika · MangochiFikitsani uthengawu ku Mangochi kwa a Mutharika: zobwelera m’boma ndi maloto chabe, a Malawi onse maso nga! pa Chakwera, watero ndi nduna ya Maboma Aang’ono a Richard Chimwendo Banda. Polankhula potsekera zokambirana mu nyumba ya malamulo lero, a Chimwendo Banda ati chipani chotsutsa cha DPP chinatuluka m’boma ndipo sichibweleranso. Iwo ati a Malawi ambiri akukumbukirabe […] The post DPP sidzabweleranso m’boma ndipo 2025 Chakwera awina ndi 70% –…See the Story
DPP sidzabweleranso m'boma ndipo 2025 Chakwera awina ndi 70% - Chimwendo Malawi 24 | Latest News from Malawi
Peter Mutharika · MalawiInu nonse amene a Peter Mutharika simukuwafuna, yang’anani kumbali. Nonse aja olemba kuti “APM my vote”, senderani chifupi. A Mutharika lero abwerezanso kuti chaka cha mawa akubwelera ku Sanjika. Mtsogoleri wa chipani chotsutsa cha DPP amene mmbuyomu amaoneka ngati wasiya za ndale asanalengezenso kuti basi akubwelera wauza anthu ku Mangochi kuti 2025 iye akuima ndipo […] The post Kaya wina afune, kaya asafune, 2025 ndikubweleranso m’boma – APM a…See the Story
Kaya wina afune, kaya asafune, 2025 ndikubweleranso m'boma - APM Malawi 24 | Latest News from Malawi
Peter Mutharika · MalawiFormer President and Democratic Progressive Party (DPP) leader Peter Mutharika has maintained he will win next year’s presidential election as the party’s candidate. Mutharika has repeated the assurance to people at Mpinganjira Village, Traditional Authority Mapira in Mangochi. He said this after donating various food stuffs to some Muslims from the area who are observing […]
The post APM donates food stuffs to Muslims in Mangochi, vows he is st…See the Story
APM donates food stuffs to Muslims in Mangochi, vows he is standing and will win
Peter Mutharika · MalawiBy Vincent Gunde Political activist Bon Elias Kalindo has warned President Dr. Lazarus McCarthy Chakwera and former President Professor Arthur Peter Mutharika that their silence not to speak against their…See the Story
Chakwera, Mutharika silence on Political Violence worrisome- Bon Kalindo
Peter Mutharika · MalawiA Undule Mwakasungula omwe ndi m’modzi mwa anthu amene amayankhulapo pa ndale ati a Peter Mutharika akuyenera aganize bwino pa lingalilo lawo lofuna kudzapikisana nawo pa mpando wa upulezidenti. A Mwakasungula ati ngakhale a Mutharika akukhulupira kuti utsogoleri wawo ndi ofunikira, pali zolepheretsa zambiri kuti adzawineso pa chisankho cha 2025. “Zaka zawo, umunthu komaso nkhani […] The post A Mutharika awapempha aganize bwino pa lingalilo lawo…See the Story