Get access to our best features
Get access to our best features
Published 2 months ago

Obera anthu ponama kuti mankhwala awo amachiza AIDS agamulidwa chindapusa cha K4.9 miliyoni Malawi 24 | Latest News from Malawi

Summary by Malawi 24
Bwalo la milandu la Senior Resident Magistrate m’boma la Mangochi, lagamula anthu awiri omwe amabera anthu ndalama pomanama kuti mankhwala omwe amagulitsa amachiza matenda a AIDS kuti alipile chindapusa cha ndalama zokwana K2,450,000 aliyese. Posachedwapa, apolisi m’boma la Mangochi anamanga mayi Mary Saidi a zaka 25 komaso a Molly Kainga powaganizira kuti akhala akubera anthu […] The post Obera anthu ponama kuti mankhwala awo amachiza AIDS agam…

0 Articles

All
Left
Center
Right
Think freely.Subscribe and get full access to Ground NewsSubscriptions start at $9.99/yearSubscribe
Ground News Article Assistant
Not enough coverage to generate an Article Assistant.

Bias Distribution

  • There is no tracked Bias information for the sources covering this story.
Factuality

To view factuality data please Upgrade to Premium

Ownership

To view ownership data please Upgrade to Vantage

Sources are mostly out of (0)