Get access to our best features
Get access to our best features
Published 2 months ago

Mayi wamangidwa pophwanya paipi yamadzi kuti atunge awulele Malawi 24 | Latest News from Malawi

Summary by Malawi 24
Apolisi ku Limbe mu mzinda wa Blantyre, akusunga m’chitokosi mzimayi wina wa zaka 21 chifukwa choononga paipi ya madzi a Blantyre Water Board mwadala ndicholinga choti atunge madzi aulele. Malingana ndi ofalitsa nkhani pa polisi ya Limbe a Aubrey Singanyama, mzimayi oganizilidwayu wazindikilidwa ngati a Celina Ganya omwe akuti anapalamula mlanduwu Lachiwiri sabata ino pa […] The post Mayi wamangidwa pophwanya paipi yamadzi kuti atunge awulele ap…

0 Articles

All
Left
Center
Right
Think freely.Subscribe and get full access to Ground NewsSubscriptions start at $9.99/yearSubscribe
Ground News Article Assistant
Not enough coverage to generate an Article Assistant.

Bias Distribution

  • There is no tracked Bias information for the sources covering this story.
Factuality

To view factuality data please Upgrade to Premium

Ownership

To view ownership data please Upgrade to Vantage

Sources are mostly out of (0)