Get access to our best features
Get access to our best features
Published 10 days ago

Agamulidwa kukakhala ku ndende kaamba koseweletsa maliseche a msungwana wachichepere Malawi 24 | Latest News from Malawi

Summary by Malawi 24
Bwalo la milandu ku Balaka, lagamula bambo wa zaka 59 zakubadwa a Steven Finye kukakhala ku ndende komanso kugagwira ntchito ya kalavula gaga kwa zaka ziwiri kaamba kopezeka olakwa pa mlandu oseweletsa maliseche a msungwana wa zaka zisanu ndi zinayi (9). Malingana ndi chikalata chochokera ku Polisi ya Balaka chomwe wasainila ndi wachiwiri kwa ofalitsa […] The post Agamulidwa kukakhala ku ndende kaamba koseweletsa maliseche a msungwana wachichepe…

0 Articles

All
Left
Center
Right
Think freely.Subscribe and get full access to Ground NewsSubscriptions start at $9.99/yearSubscribe
Ground News Article Assistant
Not enough coverage to generate an Article Assistant.

Bias Distribution

  • There is no tracked Bias information for the sources covering this story.
Factuality

To view factuality data please Upgrade to Premium

Ownership

To view ownership data please Upgrade to Vantage

Sources are mostly out of (0)