Archbishop wa mpingo wa Katolica a Thomas Msusa atsutsa zati maepikisikopi a mpingowo sakulankhula kanthu pa mavuto omwe Amalawi akkumana nawo kaamba koti adya mabanzi (adalandira ziphuphu). A Msusa adalankhula izi pa misa yomwe adachititsa pa mpingo wa St Anthony m的mzinda wa Blantyre. A Msusa kulankhula ndi atolankhani. I Nation A Archbishop amathirirapo ndemanga pa ...
This story is only covered by news sources that have yet to be evaluated by the independent media monitoring agencies we use to assess the quality and reliability of news outlets on our platform. Learn more here.